Quran Chichewa icon

Quran Chichewa

7.2

Qur'an ya Chichewa free offline.

App Information

Version
Update
Sep 23, 2020
Developer
Google Play ID
Installs
10,000+

App Names

App Description
Qur'an ya Chichewa/Chinyanja offline ikupezeka tsopano pa internet.

Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja/ Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arabic pansi pa Chichewa /Chinyanja.

Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Da'wah mma social media komanso awo omwe sabva Arabic.

Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba a mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copy and paste kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Just long click to copy and paste)

Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.
Read more